Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 23:22 - Buku Lopatulika

22 Mukanitu kuti mukadziwitse ndithu, ndi kudziwa ndi kuona mbuto m'mene akhalitsa, ndi amene adamuona m'menemo; chifukwa anandiuza kuti iye achita mochenjera ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Mukanitu kuti mukadziwitse ndithu, ndi kudziwa ndi kuona mbuto m'mene akhalitsa, ndi amene adamuona m'menemo; chifukwa anandiuza kuti iye achita mochenjera ndithu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Pitani mukaonetsetse. Mukafufuze kumene kuli mbuto yake, ndi kupeza munthu amene wamuwona chamaso kumeneko. Ndikumva kuti ngwochenjera mwaukapsala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Pitani mukatsimikizire. Mukaone kumene amakhala ndiponso mupeze munthu amene wamuona. Anthu amandiwuza kuti ndi wochenjera kwambiri.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 23:22
6 Mawu Ofanana  

Onani, tsopanoli alikubisala kudzenje kapena kwina; ndipo kudzali poyamba kugwa ena, aliyense wakumva adzanena, Alikuphedwa anthu otsata Abisalomu.


Nati iye, Kamuoneni komwe ali; ndikatume munthu kumtenga. Ndipo anamuuza kuti, Ali ku Dotani.


Akola eni nzeru m'kuchenjera kwao, ndi uphungu wa opotoka mtima usonthokera pachabe.


Saulo nati, Mudalitsike inu kwa Yehova; chifukwa munandichitira ine chifundo.


Chifukwa chake yang'anirani, ndi kudziwa ngaka zonse alikubisalamo iye, nimubwere kwa ine ndi mau otsimikizika, pomwepo ndidzamuka nanu; ndipo akakhala m'dzikomo, ndidzampwaira pakati pa mabanja onse a Yuda.


ndi kwa iwo a ku Hebroni, ndi kumalo konse kumene Davide ndi anthu ake ankayendayenda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa