1 Samueli 23:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo a ku Zifi anakwera kwa Saulo ku Gibea, nati, Davide salikubisala kwathu kodi, m'ngaka za m'nkhalango ku Horesi, m'phiri la Hakila, limene lili kumwera kwa chipululu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo a ku Zifi anakwera kwa Saulo ku Gibea, nati, Davide salikubisala kwathu kodi, m'ngaka za m'nkhalango ku Horesi, m'phiri la Hakila, limene lili kumwera kwa chipululu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Tsono anthu a ku Zifi adapita kwa Saulo ku Gibea, nakamuuza kuti, “Davide akubisala ku dera lakwathu m'mapanga a ku Horesi pa phiri la Hakila limene lili kumwera kwa Yesimoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Anthu a ku Zifi anapita kwa Sauli ku Gibeya ndipo anamuwuza kuti, “Davide akubisala kwathu, mʼmapanga a ku Horesi, mʼphiri la Hakila, kummwera kwa Yesimoni. Onani mutuwo |