1 Samueli 23:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo awiriwo anapangana pangano pamaso pa Yehova; ndipo Davide anakhala kunkhalango, koma Yonatani anapita kunyumba yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo awiriwo anapangana pangano pamaso pa Yehova; ndipo Davide anakhala kunkhalango, koma Yonatani anapita kunyumba yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pamenepo aŵiriwo adachita chipangano pamaso pa Chauta. Choncho Davide adakhalabe ku Horesi, ndipo Yonatani adabwerera kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Awiriwa anachita pangano pamaso pa Yehova. Ndipo Yonatani anabwerera kwawo, koma Davide anakhalabe ku Horesi. Onani mutuwo |