1 Samueli 23:1 - Buku Lopatulika1 Tsono anauza Davide, kuti, Onani Afilisti alikuponyana ndi Keila, nafunkha za m'madwale. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Tsono anauza Davide, kuti, Onani Afilisti alikuponyana ndi Keila, nafunkha za m'madwale. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsiku lina Davide adamva kuti Afilisti akuthira nkhondo mzinda wa Keila, ndipo akufunkha zokolola za m'nkhokwe zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Davide atawuzidwa kuti “Onani, Afilisti akuthira nkhondo mzinda wa Keila ndi kulanda zokolola zawo za mʼnkhokwe,” Onani mutuwo |