1 Samueli 22:23 - Buku Lopatulika23 Ukhale ndi ine, usaopa; popeza iye wakufuna moyo wanga afuna moyo wako; koma ndi ine udzakhala mosungika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ukhale ndi ine, usaopa; popeza iye wakufuna moyo wanga afuna moyo wako; koma ndi ine udzakhala mosungika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Koma iwe khala ndi ine, usaope ai, pakuti amene akufuna moyo wako, akufunanso moyo wanga. Ukakhala ndi ine, ukhala pabwino.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Iwe khala ndi ine, usaope munthu amene akufuna moyo wako komanso wanga. Udzatetezeka ukakhala ndi ine.” Onani mutuwo |