1 Samueli 22:9 - Buku Lopatulika9 Pamenepo Doegi wa ku Edomu, anaimirira ndi anyamata a Saulo, nayankha, nati, Ine ndinamuona mwana wa Yeseyo alikufika ku Nobu, kwa Ahimeleki mwana wa Ahitubi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pamenepo Doegi wa ku Edomu, anaimirira ndi anyamata a Saulo, nayankha, nati, Ine ndinamuona mwana wa Yeseyo alikufika ku Nobu, kwa Ahimeleki mwana wa Ahitubi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Apo Doegi Mwedomu, amene adaaimirira pafupi ndi nduna za Saulo, adanena kuti, “Ine ndidamuwona mwana wa Yese akupita ku Nobu kwa Ahimeleki, mwana wa Ahitubi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Koma Doegi Mwedomu anayima pafupi ndi nduna za Sauli nati, “Ine ndinaona mwana wa Yese atabwera kwa Ahimeleki mwana wa Ahitubi ku Nobi. Onani mutuwo |