1 Samueli 22:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo mmodzi wa ana a Ahimeleki, mwana wa Ahitubi, dzina lake ndiye Abiyatara, anapulumuka, nathawira kwa Davide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo mmodzi wa ana a Ahimeleki, mwana wa Ahitubi, dzina lake ndiye Abiyatara, anapulumuka, nathawira kwa Davide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Koma mmodzi mwa ana aamuna a Ahimeleki, mwana wa Ahitubi, dzina lake Abiyatara, adapulumuka, nathaŵa kutsatira Davide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Koma Abiatara mwana wa Ahimeleki mwana wa Ahitubi anapulumuka ndi kuthawira kwa Davide. Onani mutuwo |