1 Samueli 22:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Abiyatara anadziwitsa Davide kuti Saulo anapha ansembe a Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Abiyatara anadziwitsa Davide kuti Saulo anapha ansembe a Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Ndipo adauza Davide kuti Saulo adapha ansembe a Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Abiatara anawuza Davide kuti Sauli wapha ansembe a Yehova. Onani mutuwo |