1 Samueli 22:1 - Buku Lopatulika1 Motero Davide anachoka kumeneko, napulumukira ku phanga la ku Adulamu; ndipo pamene abale ake ndi banja lonse la atate wake anamva, iwo anatsikira kumeneko kwa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Motero Davide anachoka kumeneko, napulumukira ku phanga la ku Adulamu; ndipo pamene abale ake ndi banja lonse la atate wake anamva, iwo anatsikira kumeneko kwa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pamenepo Davide adathaŵa ku Gati, nakabisala ku phanga la Adulamu. Abale ake ndi onse a m'banja la bambo wake atamva, adapita kumene kunali Davide. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Davide anachoka kumeneko nathawira ku phanga la Adulamu. Abale ake ndi banja lonse la abambo ake anamva izi, anapita kumene kunali Davide. Onani mutuwo |