1 Samueli 21:15 - Buku Lopatulika15 Kodi ndisowa anthu amisala kuti mwabwera ndi uyu kuti akhale wamisala pamaso panga? Kodi uyu adzalowa m'nyumba mwanga? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Kodi ndisowa anthu amisala kuti mwabwera ndi uyu kuti akhale wamisala pamaso panga? Kodi uyu adzalowa m'nyumba mwanga? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Kodi ndikusoŵa anthu amisala kuti muzibwera naye kuno munthu ameneyu, namachita zamisala zake pamaso panga? Ha! Munthu wotereyu angaloŵe bwanji m'nyumba mwanga muno?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kodi ine ndikusowa anthu amisala kuti muzibwera naye munthuyu kwa ine kuti azidzachita zamisala zake pamaso panga? Kodi munthu ameneyu nʼkulowa mʼnyumba mwanga?” Onani mutuwo |