1 Samueli 21:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Davide ananyamuka, nathawa tsiku lomwelo chifukwa cha kuopa Saulo, namuka kwa Akisi mfumu ya ku Gati. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Davide ananyamuka, nathawa tsiku lomwelo chifukwa cha kuopa Saulo, namuka kwa Akisi mfumu ya ku Gati. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsiku lomwelo Davide adanyamuka kuthaŵa Saulo, ndipo adapita kwa Akisi mfumu ya ku Gati. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Tsiku lomwelo Davide ananyamuka kuthawa Sauli ndipo anapita kwa Akisi, mfumu wa ku Gati. Onani mutuwo |