1 Samueli 20:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Yonatani anati kwa Davide, Chilichonse mtima wako, unena ndidzakuchitira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Yonatani anati kwa Davide, Chilichonse mtima wako, unena ndidzakuchitira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Apo Yonatani adauza Davide kuti, “Chilichonse chimene unene, ndidzakuchitira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Yonatani anawuza Davide kuti, “Chilichonse chimene iwe ukufuna kuti ndichite, ndidzakuchitira.” Onani mutuwo |