1 Samueli 20:39 - Buku Lopatulika39 Koma mnyamatayo sanadziwe kanthu; Davide ndi Yonatani okha anadziwa za mlanduwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Koma mnyamatayo sanadziwe kanthu; Davide ndi Yonatani okha anadziwa za mlanduwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Koma mnyamatayo sadadziŵe kanthu ai, Yonatani yekha ndi Davide ndiwo amene ankadziŵa zimene zinkachitika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 (Mnyamatayo sanadziwe chimene chimachitika koma Yonatani ndi Davide ndiwo ankadziwa). Onani mutuwo |