1 Samueli 20:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo Yonatani anapatsa mnyamata wake zida zake, nanena naye, Muka, tenga izi kunka nazo kumzinda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo Yonatani anapatsa mnyamata wake zida zake, nanena naye, Muka, tenga izi kunka nazo kumudzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Choncho Yonatani adapereka zida zake kwa mnyamata wake uja, namuuza kuti, “Pita, kazitule ku mzinda.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Pambuyo pake Yonatani anapereka zida zake za nkhondo kwa mnyamatayo ndipo anati, “Pita, nyamula ubwerere nazo ku mzinda.” Onani mutuwo |