1 Samueli 20:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo Yonatani anafuulira mnyamatayo, nati, Yendetsa, fulumira, usaima. Ndi mnyamata wa Yonatani anatola mivi, nafika kwa mbuye wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo Yonatani anafuulira mnyamatayo, nati, Yendetsa, fulumira, usaima. Ndi mnyamata wa Yonatani anatola mivi, nafika kwa mbuye wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Apo Yonatani adaitananso mnyamatayo nati, “Fulumira, yenda msanga, usachedwe.” Motero mnyamata uja adatola muviwo, nabwera kwa mbuyake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 Yonatani anayitananso mnyamatayo kuti, “Fulumira, pita msanga usayime.” Choncho mnyamatayo anatola muvi uja ndi kubwera nayo kwa mbuye wake. Onani mutuwo |