1 Samueli 20:37 - Buku Lopatulika37 Ndipo mnyamatayo atafika pamalo a muvi umene Yonatani anauponya, Yonatani anafuulira mnyamatayo, nati, Muviwo suli m'tsogolo mwako kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Ndipo mnyamatayo atafika pa malo a muvi umene Yonatani anauponya, nati, Muviwo suli m'tsogolo mwako kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Ndipo mnyamatayo atafika pamalo pomwe padaagwa muviwo, Yonatani adanena chokweza kuti, “Muvi uli patsogolo pakopo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Mnyamatayo atafika pamene muvi wa Yonatani unagwera, Onani mutuwo |