1 Samueli 20:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo anauza mnyamata wakeyo, Thamanga uzikatola mivi imene ndidzaponya; ndipo analikuthamanga mnyamatayu, iye anaponya muvi kuutumphitsa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo anauza mnyamata wakeyo, Thamanga uzikatola mivi imene ndidzaponya; ndipo analikuthamanga mnyamatayu, iye anaponya muvi kuutumphitsa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Adauza mnyamata wake kuti, “Thamanga, ukatole mivi imene nditi ndiponye.” Mnyamata uja akuthamanga, Yonatani adaponya muvi patsogolo pa mnyamatayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Tsono anawuza mnyamatayo kuti, “Thamanga ukatole muvi umene nditi ndiponye.” Mnyamatayo akuthamanga Yonatani anaponya muvi patsogolo pa mnyamatayo. Onani mutuwo |