Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 20:35 - Buku Lopatulika

35 Ndipo m'mawa, Yonatani ananka kuthengoko pa nthawi imene anapangana ndi Davide, ali ndi kamnyamata.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

35 Ndipo m'mawa, Yonatani ananka kuthengoko pa nthawi imene anapangana ndi Davide, ali ndi kamnyamata.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

35 M'maŵa mwake Yonatani ndi mnyamata wake adapita kuminda kuja kumene adaapangana ndi Davide.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

35 Tsono mmawa Yonatani anapita ku munda kumene anapangana ndi Davide. Anali ndi mnyamata wake.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 20:35
4 Mawu Ofanana  

Chomwecho Amasa anamuka kukaitana anthu a Yuda asonkhane; koma anachedwa, napitiriza nthawi imene idamuikira.


Ndipo atapita masiku atatu, utsike msanga, nufike kumene unabisala tsiku la mlandu uja, nukhale pamwala wa Ezeri.


Pamenepo Yonatani anauka pagome wolunda ndithu, osadya kanthu tsiku lachiwiri la mwezi, pakuti mtima wake unali ndi chisoni chifukwa cha Davide, popeza atate wake anamchititsa manyazi.


Ndipo anauza mnyamata wakeyo, Thamanga uzikatola mivi imene ndidzaponya; ndipo analikuthamanga mnyamatayu, iye anaponya muvi kuutumphitsa iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa