1 Samueli 20:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo za chija tinakambirana iwe ndi ine, taona, Yehova ali pakati pa ife nthawi zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo za chija tinakambirana iwe ndi ine, taona, Yehova ali pakati pa ife nthawi zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Tsono pa zimene tapanganazi, Chauta ndiye mboni pakati pa ine ndi iwe mpaka muyaya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Tsono zimene tapanganazi Yehova ndiye mboni pakati pa iwe ndi ine mpaka muyaya.” Onani mutuwo |