1 Samueli 20:2 - Buku Lopatulika2 Namyankha, Usatero iai, sudzafa; ona, atate wanga sachita kanthu kakakulu kapena kakang'ono wosandidziwitsa ine; atate wanga adzandibisiranji chinthu chimenechi? Si kutero ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Namyankha, Usatero iai, sudzafa; ona, atate wanga sachita kanthu kakakulu kapena kakang'ono wosandidziwitsa ine; atate wanga adzandibisiranji chinthu chimenechi? Si kutero ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Yonatani adamuuza kuti, “Sizingatero, suufa ai. Abambo anga sachita chilichonse, chachikulu kapena chaching'ono, osandiwuza. Tsono abambo anga angandibisire bwanji zimenezi? Si choncho ai.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Yonatani anayankha kuti, “Sizitheka! Iwe sufa ayi! Taona abambo anga sachita chinthu chilichonse chachikulu kapena chachingʼono wosandiwuza ine. Tsopano abambo anga angandibisire bwanji zimenezi? Sichoncho ayi.” Onani mutuwo |