1 Samueli 20:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo atapita masiku atatu, utsike msanga, nufike kumene unabisala tsiku la mlandu uja, nukhale pamwala wa Ezeri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo atapita masiku atatu, utsike msanga, nufike kumene unabisala tsiku la mlandu uja, nukhale pa mwala wa Ezeri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Mkucha adzakufunanso kwambiri. Tsono udzapite ku malo amene udaabisala tsiku lijali, ndipo ukakhale pa mbali ina ya mulu wa miyala uli apowo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Mkuja adzakufunafuna. Tsono udzapite pamalo pamene unabisala poyamba paja ndipo ukadikire pa mulu wa miyala uli apowo. Onani mutuwo |