1 Samueli 20:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo ine ndidzaponya mivi itatu pambali pake, monga ngati ndilikuponya pachandamali. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo ine ndidzaponya mivi itatu pambali pake, monga ngati ndilikuponya pachandamali. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Ine ndidzaponya mivi itatu ku mbali ina ya muluwo, ngati ndikuchita chandamale. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ine ndidzaponya mivi itatu pambali pake, ngati ndikulasa chinthu. Onani mutuwo |