1 Samueli 20:18 - Buku Lopatulika18 Tsono Yonatani ananena kwa Davide, Mawa mwezi ukhala; ndipo adzakufuna, popeza udzasoweka pamalo pako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Tsono Yonatani ananena kwa Davide, Mawa mwezi ukhala; ndipo adzakufuna, popeza udzasoweka pamalo pako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Tsono Yonatani adatinso, “Maŵa mwezi ukhala, ndipo pa phwando adzazindikira kuti iwe palibe, popeza kuti pampando pako padzakhala popanda munthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Kenaka Yonatani anawuzanso Davide kuti, “Mawa ndi tsiku la chikondwerero cha mwezi watsopano. Zidzadziwika kuti iwe palibe chifukwa mpando wako udzakhala wopanda munthu. Onani mutuwo |