1 Samueli 20:15 - Buku Lopatulika15 komanso usaleke kuchitira chifundo a m'nyumba yanga nthawi zonse: mungakhale m'tsogolomo Yehova atathera adani onse a Davide padziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 komanso usaleke kuchitira chifundo a m'nyumba yanga nthawi zonse: mungakhale m'tsogolomo Yehova atathera adani onse a Davide pa dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pamene Chauta adzaŵatha adani onse a Davide pa dziko lapansi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ndipo usadzaleke kuchitira chifundo banja langa. Pamene Yehova adzawatha adani onse a Davide pa dziko lapansi.” Onani mutuwo |