1 Samueli 20:13 - Buku Lopatulika13 Mulungu alange Yonatani, ndi kuonjezapo, ngati atate wanga akondwera kukuchitira choipa, ine osakuululira, ndi kukuchotsa kuti upite mumtendere; ndipo Yehova akhale nawe, monga anakhala naye atate wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Mulungu alange Yonatani, ndi kuonjezapo, ngati atate wanga akondwera kukuchitira choipa, ine osakuululira, ndi kukuchotsa kuti upite mumtendere; ndipo Yehova akhale nawe, monga anakhala naye atate wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Koma akakafunitsitsa kukuchita choipa, Chauta adzandilange kwambiri ndikapanda kukuululira ndi kukuthandiza kuti upulumuke. Chauta akhale nawe, monga momwe adakhalira ndi abambo anga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Koma ngati abambo anga atsimikiza kukuchita choyipa, Yehova andilange ine Yonatani, ndipotu kwambiri ngati sindidzakudziwitsa ndi kukulola kuti upite mu mtendere. Yehova akhale nawe monga anakhalira ndi abambo anga. Onani mutuwo |