1 Samueli 20:11 - Buku Lopatulika11 Nati Yonatani kwa Davide, Tiyeni timuke kuthengo. Namuka onse awiri kuthengoko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Nati Yonatani kwa Davide, Tiyeni timuke kuthengo. Namuka onse awiri kuthengoko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Yonatani adayankha kuti, “Tiye tikayende chakumindaku.” Choncho onse aŵiriwo adapita kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Yonatani anawuza Davide kuti, “Tiyeni tikayende ku mundako.” Ndipo anapita onse awiri. Onani mutuwo |