1 Samueli 20:10 - Buku Lopatulika10 Tsono Davide anati kwa Yonatani, Adzandiuza ndani ngati atate wako alankhulira iwe mokalipa? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Tsono Davide anati kwa Yonatani, Adzandiuza ndani ngati atate wako alankhulira iwe mokalipa? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Apo Davide adafunsa Yonatani kuti, “Kodi ndani amene adzandiwuze, abambo ako akakuyankha mokalipa?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Davide anafunsa kuti, “Adzandiwuza ndani ngati abambo ako akuyankhe mwaukali?” Onani mutuwo |