1 Samueli 2:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Elikana ananka kwao ku Rama, mwanayo natumikira Yehova pamaso pa Eli wansembeyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Elikana ananka kwao ku Rama, mwanayo natumikira Yehova pamaso pa Eli wansembeyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsono Elikana adabwerera kwao ku Rama. Koma mnyamata uja Samuele adatsala, ndipo ankatumikira Chauta pamaso pa wansembe Eli. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tsono Elikana anapita ku mudzi kwawo ku Rama, koma mnyamatayo amatumikira Yehova pansi pa ulamuliro wa wansembe Eli. Onani mutuwo |