1 Samueli 2:12 - Buku Lopatulika12 Koma ana a Eli anali oipa; sanadziwe Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma ana a Eli anali oipa; sanadziwe Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono ana a Eli anali achabechabe, sankasamalako za Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ana a Eli anali ana achabechabe pakuti samasamala za Yehova. Onani mutuwo |