1 Samueli 19:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo mzimu woipa wochokera kwa Yehova unali pa Saulo, pakukhala iye m'nyumba mwake, ndi mkondo wake m'dzanja lake; ndipo Davide anaimba ndi dzanja lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo mzimu woipa wochokera kwa Yehova unali pa Saulo, pakukhala iye m'nyumba mwake, ndi mkondo wake m'dzanja lake; ndipo Davide anaimba ndi dzanja lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsiku lina mzimu woipa uja udatsikira Saulo pa nthaŵi yomwe anali m'nyumba mwake, mkondo uli m'manja, Davide akuimba zeze. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Tsiku lina mzimu woyipa uja unafikanso pa Sauli. Nthawi imeneyi nʼkuti Sauli uja ali mʼnyumba mwake, mkondo uli mʼdzanja lake ndi Davide akuyimba zeze, Onani mutuwo |