1 Samueli 19:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo kunalinso nkhondo; ndipo Davide anatuluka, nakamenyana ndi Afilisti, nawapha ndi maphedwe aakulu, ndipo iwo anamthawa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo kunalinso nkhondo; ndipo Davide anatuluka, nakamenyana ndi Afilisti, nawapha ndi maphedwe akulu, ndipo iwo anamthawa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Nkhondo ina idabukanso. Davide adapita kukamenyana ndi Afilisti. Adapha Afilisti ambiri, kotero kuti iwowo adathaŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Panabukanso nkhondo ina ndipo Davide anapita ndi kukamenyana ndi Afilisti. Iye anawakantha mwamphamvu kotero kuti Afilisti anathawa. Onani mutuwo |