1 Samueli 19:22 - Buku Lopatulika22 Pamenepo iyenso anamuka ku Rama, nafika ku chitsime chachikulu chili ku Seku, nafunsa nati, Samuele ndi Davide ali kuti? Ndipo wina anati, Taonani, ali ku Nayoti mu Rama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Pamenepo iyenso anamuka ku Rama, nafika ku chitsime chachikulu chili ku Seku, nafunsa nati, Samuele ndi Davide ali kuti? Ndipo wina anati, Taonani, ali ku Nayoti m'Rama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Choncho Saulo mwini wake adanyamuka napita ku Rama, nakafika pa chitsime chachikulu chimene chili ku Seku. Ndipo adafunsa kuti, “Kodi Samuele ndi Davide ali kuti?” Munthu wina adati, “Ali ku Nayoti ku Rama.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Pomaliza Sauli mwini wake ananyamuka kupita ku Rama ndipo anafika ku chitsime chachikulu cha ku Seku. Ndipo anafunsa, “Samueli ndi Davide ali kuti?” Munthu wina anamuyankha kuti, “Ali ku Nayoti ku Rama.” Onani mutuwo |