Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 19:21 - Buku Lopatulika

21 Ndipo pamene anauza Saulo, iye anatumiza mithenga ina; koma iyonso inanenera. Ndipo Saulo anatumiza mithenga kachitatu, nayonso inanenera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ndipo pamene anauza Saulo, iye anatumiza mithenga ina; koma iyonso inanenera. Ndipo Saulo anatumiza mithenga kachitatu, nayonso inanenera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Saulo atazimva zimenezo, adatuma anthu ena, ndipo nawonso adayamba kulosa. Adatumanso anthu ena kachitatu, nawonso adayamba kulosa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Sauli atamva zimenezi anatumizanso anthu ena, koma nawonso anayamba kulosa. Anatumanso anthu ena kachitatu, koma nawonso anayamba kulosa.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 19:21
6 Mawu Ofanana  

Ungakhale ukonola chitsiru m'mtondo ndi munsi, pamodzi ndi mphale, koma utsiru wake sudzamchoka.


Kodi angathe Mkusi kusanduliza khungu lake, kapena nyalugwe mawanga ake? Pamenepo mungathe inunso kuchita zabwino, inu amene muzolowera kuchita zoipa.


Ndipo kudzachitika m'tsogolo mwake, ndidzatsanulira mzimu wanga pa anthu onse, ndi ana aamuna ndi aakazi adzanenera, akuluakulu anu adzalota maloto, anyamata anu adzaona masomphenya;


Ndipo Saulo anatumiza mithenga kuti igwire Davide, ndipo pamene inaona gulu la aneneri alikunenera, ndi Samuele mkulu wao alikuimapo, mzimu wa Mulungu unagwera mithenga ya Saulo, ninenera iyonso.


Pamenepo iyenso anamuka ku Rama, nafika ku chitsime chachikulu chili ku Seku, nafunsa nati, Samuele ndi Davide ali kuti? Ndipo wina anati, Taonani, ali ku Nayoti mu Rama.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa