1 Samueli 19:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo pamene Saulo anatumiza mithenga kuti ikamgwire Davide, anati, Iye alikudwala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo pamene Saulo anatumiza mithenga kuti ikamgwire Davide, anati, Iye alikudwala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Pamene anthu a Saulo aja adafika kuti adzamgwire Davide, Mikala adati, “Davide akudwala.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Pamene amithenga a Sauli aja anafika kuti akamugwire Davide, Mikala anati, “Davide akudwala.” Onani mutuwo |