Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 19:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo Saulo anatumiza mithengayo kuti ikaone Davide, nati, Mumtengere iye pa kama wake, kuti ndidzamuphe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo Saulo anatumiza mithengayo kuti ikaone Davide, nati, Mumtengere iye pa kama wake, kuti ndidzamuphe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Koma Saulo adaŵatumanso anthuwo kuti akamgwire ndithu Davideyo. Adaŵauza kuti, “Mubwere naye kuno, mumnyamulire pabedi pomwepo kuti ndidzamuphe.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Koma Sauli anatumanso anthuwo kuti akamuone Davide, nati, “Mubwere naye kuno ali pa bedi pomwepo kuti ndidzamuphe.”

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 19:15
7 Mawu Ofanana  

Ngati amuna a m'hema mwanga sanati, ndani adzapeza munthu wosakhuta nyama yomgawira Yobu?


Woipa apangira chiwembu wolungama, namkukutira mano.


miyendo yao ichita liwiro kukhetsa mwazi;


Ndipo pamene Saulo anatumiza mithenga kuti ikamgwire Davide, anati, Iye alikudwala.


Ndipo pakulowa mithengayo, onani, pakama pali chifanizo ndi mtsamiro wa ubweya wa mbuzi kumutu kwake.


Ndipo Saulo anamvera mau a Yonatani; nalumbira, Pali Yehova, sadzaphedwa iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa