1 Samueli 19:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo pakulowa mithengayo, onani, pakama pali chifanizo ndi mtsamiro wa ubweya wa mbuzi kumutu kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo pakulowa mithengayo, onani, pakama pali chifanizo ndi mtsamiro wa ubweya wa mbuzi kumutu kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Anthuwo atakaloŵa, adangoona fano pabedipo ndi mtsamiro wa ubweya wambuzi kumutu kwake kwa fanolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Koma pamene anthuwo analowa, anangoona fano pa bedipo ndi pilo wa ubweya wa mbuzi ku mutu kwake. Onani mutuwo |