1 Samueli 19:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Mikala anatenga terafi namuika pakama, naika mtsamiro wa ubweya wa mbuzi kumutu kwake, nachifunda zofunda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Mikala anatenga chifanizo nachiika pakama, naika mtsamiro wa ubweya wa mbuzi kumutu kwake, nachifunda zofunda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mikalayo adatenga fano lam'nyumba naligoneka pa bedi, naika mtsamiro wa ubweya wambuzi kumutu kwake kwa fanolo, nalifunditsa nsalu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Kenaka Mikala anatenga fano naligoneka pa bedi nayika pilo wa ubweya wa mbuzi ku mutu kwa fanolo ndipo analifunditsa nsalu. Onani mutuwo |