1 Samueli 19:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Saulo analankhula kwa Yonatani mwana wake, ndi anyamata ake onse kuti amuphe Davide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Saulo analankhula kwa Yonatani mwana wake, ndi anyamata ake onse kuti amuphe Davide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Saulo adalamula mwana wake Yonatani ndi akuluakulu onse kuti aphe Davide. Koma Yonatani ankakonda Davide kwambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Sauli anawuza mwana wake Yonatani ndi nduna zake zonse kuti aphe Davide. Koma Yonatani amamukonda kwambiri Davide. Onani mutuwo |