1 Samueli 19:2 - Buku Lopatulika2 Koma Yonatani mwana wa Saulo anakondwera kwambiri ndi Davide. Ndipo Yonatani anauza Davide, nati, Saulo atate wanga alikufuna kukupha; chifukwa chake tsono uchenjere m'mawa, mukhale m'malo mosadziwika, nubisale; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Koma Yonatani mwana wa Saulo anakondwera kwambiri ndi Davide. Ndipo Yonatani anauza Davide, nati, Saulo atate wanga alikufuna kukupha; chifukwa chake tsono uchenjere m'mawa, mukhale m'malo mosadziwika, nubisale; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Choncho adakauza Davide kuti, “Iwe, abambo anga akufuna kukupha. Ndiye uchenjere, m'maŵa ukakhale kwina kobisalika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Choncho anawuza Davide kuti, “Abambo anga Sauli akufuna kukupha. Tsono uchenjere. Mmawa upite ukabisale ndipo ukakhale komweko. Onani mutuwo |