1 Samueli 18:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Yonatani anavula malaya ake anali nao, napatsa Davide, ndi zovala zake, ngakhale lupanga lake, ndi uta wake, ndi lamba lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Yonatani anavula malaya ake anali nao, napatsa Davide, ndi zovala zake, ngakhale lupanga lake, ndi uta wake, ndi lamba lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono adavula mwinjiro umene anali nawo napatsa Davide pamodzi ndi zovala zankhondo, lupanga lake, uta wake ndi lamba wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Yonatani anavula mkanjo umene anavala ndipo anamupatsa Davide pamodzi ndi zovala za nkhondo, lupanga, uta ndi lamba. Onani mutuwo |