1 Samueli 18:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo Davide anatuluka kunka kulikonse Saulo anamtumako, nakhala wochenjera; ndipo Saulo anamuika akhale woyang'anira anthu a nkhondo; ndipo ichi chinakomera anthu onse, ndi anyamata a Saulo omwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Davide anatuluka kunka kulikonse Saulo anamtumako, nakhala wochenjera; ndipo Saulo anamuika akhale woyang'anira anthu a nkhondo; ndipo ichi chinakomera anthu onse, ndi anyamata a Saulo omwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Tsono kulikonse kumene Davide ankatumidwa ndi Saulo kuti akamenye nkhondo, ankapambana adani. Motero Saulo adamuika Davide kuti akhale mtsogoleri wa ankhondo. Chimenechi chidakondwetsa anthu onse, ngakhalenso atsogoleri a ankhondo a Saulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Davide ankapita kulikonse kumene Sauli ankamutuma kuti apite kukamenya nkhondo, ndipo ankapambana. Choncho Sauli anamupatsa udindo woyangʼanira gulu lankhondo. Ichi chinakondweretsa anthu onse ngakhalenso atsogoleri a nkhondo a Sauli. Onani mutuwo |