1 Samueli 18:3 - Buku Lopatulika3 Pamenepo Yonatani ndi Davide anapangana pangano, pakuti adamkonda iye ngati moyo wa iye yekha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pamenepo Yonatani ndi Davide anapangana pangano, pakuti adamkonda iye ngati moyo wa iye yekha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Adachita naye chipangano chifukwa ankamkonda monga momwe ankadzikondera iye mwini. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndipo Yonatani anapanga pangano ndi Davide chifukwa ankamukonda monga momwe ankadzikondera. Onani mutuwo |