1 Samueli 18:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Saulo anamtenga tsiku lomwelo, osamlolanso apite kwao kwa atate wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Saulo anamtenga tsiku lomwelo, osamlolanso apite kwao kwa atate wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mwakuti adamtenga Davideyo tsiku lomwelo, osamlola kuti abwerere ku banja kwa bambo wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Choncho Sauli anamusunga Davideyo kuyambira tsiku limenelo ndipo sanamulole kuti abwerere ku nyumba ya abambo ake. Onani mutuwo |