1 Samueli 18:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo Saulo anaona, nadziwa kuti Yehova ali ndi Davide; ndi kuti Mikala mwana wa Saulo anamkonda Davide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo Saulo anaona, nadziwa kuti Yehova ali ndi Davide; ndi kuti Mikala mwana wa Saulo anamkonda Davide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Koma Saulo atazindikira kuti Chauta ali naye Davide, ndiponso kuti mwana wake Mikala ankamkonda Davideyo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Sauli atazindikira kuti Yehova anali ndi Davide ndiponso kuti mwana wake Mikala amamukonda Davide, Onani mutuwo |