1 Samueli 18:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo pamene anyamata ake anauza Davide mau awa, kudamkomera Davide kukhala mkamwini wa mfumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo pamene anyamata ake anauza Davide mau awa, kudamkomera Davide kukhala mkamwini wa mfumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Ndiye nduna za Saulozo zitamuuza Davide mau ameneŵa, zidamkondweretsa kuti akhale mkamwini wa mfumu. Nthaŵi yoti atenge mkazi wake isanakwane, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Nduna za Saulizo zitamuwuza Davide zimenezi, anakondwera kuti akhale mpongozi wa mfumu. Koma nthawi imene anapatsidwa isanathe, Onani mutuwo |