1 Samueli 18:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo anyamata a Saulo anamuuza, kuti, Anatero Davide. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo anyamata a Saulo anamuuza, kuti, Anatero Davide. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Nduna za Saulo zidamuuza zonse zimene Davide adaanena. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Nduna za Sauli zinamuwuza zonse zimene anayankha Davide. Onani mutuwo |