Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 18:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo pamene Saulo anaona kuti analikukhala wochenjera ndithu anamuopa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo pamene Saulo anaona kuti analikukhala wochenjera ndithu anamuopa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Tsono pamene Saulo adaona kuti Davide akupambana kwambiri, adayamba kuchita naye mantha.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Sauli ataona momwe Davide ankapambanira, iye anamuopa kwambiri.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 18:15
8 Mawu Ofanana  

Wodala munthu wakuchitira chifundo, nakongoletsa; adzalimbika nao mlandu wake poweruzidwa.


Muyendere munzeru ndi iwo akunja, kuchita machawi nthawi ingatayike.


Koma wina wa inu ikamsowa nzeru, apemphe kwa Mulungu, amene apatsa kwa onse modzala manja, niwosatonza; ndipo adzampatsa iye.


Koma nzeru yochokera kumwamba iyamba kukhala yoyera, nikhalanso yamtendere, yaulere, yomvera bwino, yodzala chifundo ndi zipatso zabwino, yopanda tsankho, yosadzikometsera pamaso.


Ndipo Saulo anaopa Davide chifukwa Yehova anali naye, koma adamchokera Saulo.


Ndipo Davide anakhala wochenjera m'mayendedwe ake onse; ndipo Yehova anali naye.


Koma Aisraele onse ndi Ayuda onse anamkonda Davide pakuti anawatsogolera kutuluka ndi kulowa nao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa