1 Samueli 17:9 - Buku Lopatulika9 Akakhoza iyeyo kuponyana ndi ine ndi kundipha, tidzakhala ife akapolo anu; koma ine ndikamgonjetsa ndi kumupha, tsono mudzakhala inu akapolo athu, ndi kutitumikira ife. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Akakhoza iyeyo kuponyana ndi ine ndi kundipha, tidzakhala ife akapolo anu; koma ine ndikamlaka, ndi kumupha, tsono mudzakhala inu akapolo athu, ndi kutitumikira ife. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ngati angathe kulimbana nane ndi kundipha, ndiye kuti Afilisti tonse tidzakhala akapolo anu. Koma ndikampambana ndi kumupha, inuyo mudzakhala akapolo athu ndi kumatigwirira ntchito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ngati angathe kumenyana nane ndi kundipha, ife tidzakhala akapolo anu, koma ngati ine ndimugonjetsa ndi kumupha, inu mudzakhala akapolo athu ndi kumatitumikira.” Onani mutuwo |