1 Samueli 17:10 - Buku Lopatulika10 Nati Mfilistiyo, Ine ndinyoza makamu a nkhondo a Israele lero; mundipatse munthu, kuti tilimbane ife awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Nati Mfilistiyo, Ine ndinyoza makamu a nkhondo a Israele lero; mundipatse munthu, kuti tilimbane ife awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tiwonane lero lino basi! Patseni munthu kuti ndimenyane naye.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndipo Mfilisitiyo anati, “Bwerani lero timenyane basi! Patseni munthu kuti ndimenyane naye.” Onani mutuwo |