1 Samueli 17:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo pamene Saulo ndi Aisraele onse anamva mau ao a Mfilistiyo, anadodoma, naopa kwambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo pamene Saulo ndi Aisraele onse anamva mau ao a Mfilistiyo, anadodoma, naopa kwambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Atamva mau a Mfilistiyo, Saulo ndi Aisraele onse adachita mantha nathyoka m'nkhongono. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Atamva mawu a Mfilisitiyo, Sauli ndi Aisraeli onse anataya mtima nachita mantha kwambiri. Onani mutuwo |